Ekisodo 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+ Ekisodo 40:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anasanja mkate woonetsa+ Yehova patebulopo, monga mmene Yehova analamulira Mose.