Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Lamulo lililonse ligwire ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+

  • Levitiko 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+

  • Deuteronomo 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ana anu, akazi anu,+ alendo+ okhala mkati mwa msasa wanu, kuyambira wokutolerani nkhuni mpaka wokutungirani madzi,+

  • Deuteronomo 31:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi.

  • Aroma 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Mulungu alibe tsankho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena