Deuteronomo 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+ Deuteronomo 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 yokhalanso ndi anthu amphamvu ndi aatali, ana a Anaki,+ amene inu mukuwadziwa ndipo munamva anthu akunena za iwo kuti, ‘Ndani angaime pamaso pa ana a Anaki?’
28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+
2 yokhalanso ndi anthu amphamvu ndi aatali, ana a Anaki,+ amene inu mukuwadziwa ndipo munamva anthu akunena za iwo kuti, ‘Ndani angaime pamaso pa ana a Anaki?’