Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 13:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+

  • Deuteronomo 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+

  • Deuteronomo 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anthu amenewa anali amphamvu kwambiri ndiponso ochuluka. Analinso ataliatali ngati Aanaki.+ Yehova anawafafaniza+ kuwachotsa pamaso pa ana a Amoni kuti ana a Amoniwo atenge dzikolo ndi kukhalamo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena