Numeri 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+ Deuteronomo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 (Kale munali kukhala Aemi,+ anthu amphamvu kwambiri ndiponso ochuluka. Iwo anali ataliatali ngati Aanaki.+ Deuteronomo 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 yokhalanso ndi anthu amphamvu ndi aatali, ana a Anaki,+ amene inu mukuwadziwa ndipo munamva anthu akunena za iwo kuti, ‘Ndani angaime pamaso pa ana a Anaki?’
33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+
10 (Kale munali kukhala Aemi,+ anthu amphamvu kwambiri ndiponso ochuluka. Iwo anali ataliatali ngati Aanaki.+
2 yokhalanso ndi anthu amphamvu ndi aatali, ana a Anaki,+ amene inu mukuwadziwa ndipo munamva anthu akunena za iwo kuti, ‘Ndani angaime pamaso pa ana a Anaki?’