Numeri 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+ Yoswa 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zisanachitike, mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba+ (Ariba+ anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki). Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+
33 Tinaonakonso Anefili,* mbadwa za Anaki,+ moti eni akefe tinangodziona ngati tiziwala kwa iwo. Iwonso ndi mmene anationera.”+
15 Zimenezi zisanachitike, mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba+ (Ariba+ anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki). Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+