Levitiko 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+ Yoswa 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Yoswa analanda dziko lonse monga mmene Yehova analonjezera Mose.+ Ndiyeno Yoswa anapereka dzikolo kwa Aisiraeli monga cholowa chawo, malinga ndi magawo awo potsata mafuko awo.+ Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+
6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+
23 Chotero Yoswa analanda dziko lonse monga mmene Yehova analonjezera Mose.+ Ndiyeno Yoswa anapereka dzikolo kwa Aisiraeli monga cholowa chawo, malinga ndi magawo awo potsata mafuko awo.+ Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+