Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+ Numeri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli, uwauze kuti, ‘Pamene mukukalowa m’dziko la Kanani,+ nawa malire a dziko+ limene mudzalandire ngati cholowa chanu.+ Deuteronomo 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova adzachotsa mitundu yonseyi chifukwa cha inu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+
27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+
2 “Lamula ana a Isiraeli, uwauze kuti, ‘Pamene mukukalowa m’dziko la Kanani,+ nawa malire a dziko+ limene mudzalandire ngati cholowa chanu.+
23 Yehova adzachotsa mitundu yonseyi chifukwa cha inu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+