Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Anachita izi kuti achotse mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, ndi kulowetsamo inu, kukupatsani dziko lawo kuti likhale cholowa chanu monga mmene zilili lero.+

  • Yoswa 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu ndi ku Lebanoni uyu mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu, kolowera dzuwa.+

  • Yoswa 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+

  • Yeremiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ine ndanena kuti, ‘Mokondwera ndinakuikani pakati pa ana anga ndi kukupatsani dziko labwino,+ cholowa chimene mitundu yambiri ya anthu imachisirira!’ Ndipo ndinanenanso kuti, ‘Anthu inu mudzandiitana kuti, “Atate wanga!”+ ndipo mudzandilondola osabwerera.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena