Ekisodo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wankhondo.+ Dzina lake ndi Yehova.+ Salimo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+
8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+