Salimo 62:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kawiri konse ndamva kuti Mulungu wanena kuti,+Mphamvu ndi za Mulungu.+ Salimo 147:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+Nzeru zake zilibe malire.+