Yobu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+Ndani angachite naye makani,* koma osavulala?+ Salimo 63:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho ndakuonani m’malo oyera,+Chifukwa ndaona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.+ Salimo 77:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+ Nahumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+ Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+
14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+
3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+
19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+