Yoswa 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsiku lotsatira, iwo anayamba kudya zokolola za m’dzikomo. Pa tsikuli anayamba kudya mikate yopanda chofufumitsa+ ndiponso tirigu wokazinga. Yoswa 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+
11 Tsiku lotsatira, iwo anayamba kudya zokolola za m’dzikomo. Pa tsikuli anayamba kudya mikate yopanda chofufumitsa+ ndiponso tirigu wokazinga.
12 Mana analeka kugwa pa tsikuli, pamene ana a Isiraeli anadya zokolola za m’dzikomo. Kuyambira pamenepo, mana sanagwenso pakati pa ana a Isiraeli.+ Chotero, chaka chimenechi n’chimene iwo anayamba kudya zokolola za m’dziko la Kanani.+