Ekisodo 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo ana aamuna a Izara anali Kora,+ Nefegi ndi Zikiri. Numeri 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Kohati,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli.