Numeri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire. Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+ Numeri 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+
16 Tsopano Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani+ ndi Abiramu+ ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire.
32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+
10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+