Ekisodo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137. Numeri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Levi+ anali awa: Gerisoni, Kohati ndi Merari.+
16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.