Numeri 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani+ ndi Abiramu.+ Awiriwa, Datani ndi Abiramu, anali osankhidwa a khamulo. Iwowa ndi amene anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose ndi Aroni, pamene anali kutsutsana ndi Yehova. Numeri 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna. Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+
9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani+ ndi Abiramu.+ Awiriwa, Datani ndi Abiramu, anali osankhidwa a khamulo. Iwowa ndi amene anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose ndi Aroni, pamene anali kutsutsana ndi Yehova.
3 “Bambo athu anafera m’chipululu.+ Koma iwo sanali nawo m’gulu la Kora+ limene linasonkhana kuti litsutsane ndi Yehova. Bambo athuwo anafa chifukwa cha tchimo lawo,+ ndipo pa nthawiyo analibe mwana aliyense wamwamuna.
11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+