Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndipo Aroni ndi ana ake adye+ nyama ya nkhosayo ndi mkate umene uli m’dengu, adyere pakhomo la chihema chokumanako.

  • Levitiko 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.

  • Levitiko 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mudye nsembeyo m’malo oyera,+ chifukwa ndi gawo lanu komanso ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Zimenezi n’zimene ndalamulidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena