Levitiko 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’” Levitiko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+
18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”
6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+