Ekisodo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana aliyense woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa, koma ngati simungamuwombole, muzimupha mwa kum’thyola khosi.+ Ndipo aliyense woyamba kubadwa mwa ana anu aamuna muzimuwombola.+
13 Mwana aliyense woyamba kubadwa wa bulu muzimuwombola ndi nkhosa, koma ngati simungamuwombole, muzimupha mwa kum’thyola khosi.+ Ndipo aliyense woyamba kubadwa mwa ana anu aamuna muzimuwombola.+