15 “Chamoyo chilichonse chotsegula mimba ya mayi ake,+ chimene chiziperekedwa kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe, uzionetsetsa kuti ukuwombola mwana woyamba kubadwa wa munthu.+ Uziwombolanso+ mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.