Salimo 147:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Machitidwe 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’mibadwo ya m’mbuyomu iye analola anthu a mitundu yonse kuyenda m’njira zawo.+
20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.+Tamandani Ya, anthu inu!+