Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+

  • Ekisodo 31:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chimenechi n’chizindikiro pakati pa ine ndi ana a Isiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa m’masiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake.’”+

  • Deuteronomo 4:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Tafunsani tsopano, za masiku akale+ inu musanakhalepo, kuchokera pa tsiku limene Mulungu analenga munthu padziko lapansi,+ ndiponso kuchokera kumalekezero ena a thambo kukafika kumalekezero ena a thambo, Kodi chinthu chachikulu ngati chimenechi chinayamba chachitikapo, kapena kodi chinthu ngati chimenechi chinayamba chamvekapo?+

  • Deuteronomo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+

  • Aroma 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye amaposadi ena kwambiri m’njira iliyonse. Choyamba, chifukwa chakuti mawu opatulika a Mulungu+ anaikidwa m’manja mwa Ayuda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena