Ekisodo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zitatero Mose anatulutsa anthuwo mumsasa kuti akakumane ndi Mulungu woona, ndipo anapita kukaima m’tsinde mwa phirilo.+ Deuteronomo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene chala cha Mulungu chinalembapo.+ Pamiyala iwiri imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu m’phiri, kuchokera pakati pa moto, tsiku limene munasonkhana kumeneko.+
17 Zitatero Mose anatulutsa anthuwo mumsasa kuti akakumane ndi Mulungu woona, ndipo anapita kukaima m’tsinde mwa phirilo.+
10 ndipo Yehova anandipatsa miyala iwiri yosema imene chala cha Mulungu chinalembapo.+ Pamiyala iwiri imeneyi panali mawu onse amene Yehova analankhula nanu m’phiri, kuchokera pakati pa moto, tsiku limene munasonkhana kumeneko.+