Numeri 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Oweruzawo+ alanditse wakupha munthuyo m’manja mwa wobwezera magazi, ndipo am’bwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika+ adzamwalire.
25 Oweruzawo+ alanditse wakupha munthuyo m’manja mwa wobwezera magazi, ndipo am’bwezere kumzinda wothawirako kumene anathawira. Iye ayenera kukhala mumzindamo mpaka mkulu wa ansembe amene anadzozedwa ndi mafuta opatulika+ adzamwalire.