Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+ Levitiko 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+ Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+