Deuteronomo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi, mwakuti wamuipitsira mbiri+ yake ponena kuti, ‘Ine ndinatenga mkazi uyu ndi kugona naye, koma sindinapeze umboni uliwonse woti anali namwali.’+ Deuteronomo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pano akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi+ kuti: “Ndaona kuti palibe umboni wosonyeza kuti mwana wanuyu anali namwali.”+ Koma nawu umboni wa unamwali wa mwana wanga.’ Pamenepo azifunyulula chofunda pamaso pa akulu a mzinda.
14 ndipo akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi, mwakuti wamuipitsira mbiri+ yake ponena kuti, ‘Ine ndinatenga mkazi uyu ndi kugona naye, koma sindinapeze umboni uliwonse woti anali namwali.’+
17 Pano akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi+ kuti: “Ndaona kuti palibe umboni wosonyeza kuti mwana wanuyu anali namwali.”+ Koma nawu umboni wa unamwali wa mwana wanga.’ Pamenepo azifunyulula chofunda pamaso pa akulu a mzinda.