-
Deuteronomo 22:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 ndipo akumuimba mlandu wochita khalidwe loipa komanso wamuipitsira mbiri yake ponena kuti: ‘Ine ndinatenga mkazi uyu koma nditagona naye, sindinapeze umboni uliwonse woti anali namwali.’
-