Deuteronomo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi, mwakuti wamuipitsira mbiri+ yake ponena kuti, ‘Ine ndinatenga mkazi uyu ndi kugona naye, koma sindinapeze umboni uliwonse woti anali namwali.’+
14 ndipo akumuimba mlandu wochita zinthu zonyansa ndi zochititsa manyazi, mwakuti wamuipitsira mbiri+ yake ponena kuti, ‘Ine ndinatenga mkazi uyu ndi kugona naye, koma sindinapeze umboni uliwonse woti anali namwali.’+