Salimo 107:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kumeneko amakhazikako anthu anjala,+Kuti amange mzinda woti azikhalamo.+