Salimo 146:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+ Luka 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino,+ amene anali ndi chuma wawapitikitsa chimanjamanja.+
7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+