Luka 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino+ koma amene anali ndi chuma wawathamangitsa chimanjamanja. 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Mariya analemekeza Yehova (gnj 1 21:14–24:00)
53 Wakhutitsa anthu anjala ndi zinthu zabwino+ koma amene anali ndi chuma wawathamangitsa chimanjamanja.