1 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.* Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa iye wathetsa ludzu la anthu aludzuNdipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+
5 Odya bwino ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,Koma anjala alibenso njala.+ Wosabereka wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, ali yekhayekha.*
10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+