1 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anali okhuta ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,+Koma anjala, njala yawo yawathera.+ Ngakhale wosabereka, wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, wasiya kubereka.+ Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wapereka madzi kwa anthu aludzu.+Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+
5 Amene anali okhuta ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,+Koma anjala, njala yawo yawathera.+ Ngakhale wosabereka, wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, wasiya kubereka.+
10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+