Levitiko 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+ Yeremiya 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzapha onse okhala mumzinda uwu, anthu ndi nyama zomwe. Adzafa ndi mliri waukulu.”’+ Yeremiya 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+
25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+
10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+