Levitiko 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+ 2 Mbiri 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 tamvera tsopano! Yehova adzalanga mwamphamvu+ anthu ako,+ ana ako+ ndi akazi ako, ndipo adzawononga katundu wako yense. Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+
21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+
14 tamvera tsopano! Yehova adzalanga mwamphamvu+ anthu ako,+ ana ako+ ndi akazi ako, ndipo adzawononga katundu wako yense.
12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+