Hoseya 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onsewo akutentha ngati ng’anjo yamoto, ndipo akuwononga oweruza awo. Mafumu awo onse agwa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akundiitana.+
7 Onsewo akutentha ngati ng’anjo yamoto, ndipo akuwononga oweruza awo. Mafumu awo onse agwa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akundiitana.+