9 Pambuyo pake, Abulamu anasamutsa hema wake kumeneko. Kuyambira pa nthawi imeneyi, iye ankangokhalira kumanga ndi kusamutsa msasa, kulowera ku Negebu.+
21Tsopano mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inali kukhala ku Negebu,+ inamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu. Itamva zimenezo inapita kukamenyana nawo ndipo Aisiraeli ena inawagwira ndi kupita nawo kudziko lake.