Deuteronomo 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Onani, ndikukuikirani pamaso panu lero dalitso ndi temberero:+ Deuteronomo 32:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+
47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+