Yoswa 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa umu ndi mmene Yehova azichitira ndi adani anu onse amene mukumenyana nawo.”+ Aefeso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Potsiriza ndikuti, pitirizani kupeza mphamvu+ kuchokera kwa Ambuye ndiponso kuchokera ku mphamvu+ zake zazikulu.
25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa umu ndi mmene Yehova azichitira ndi adani anu onse amene mukumenyana nawo.”+
10 Potsiriza ndikuti, pitirizani kupeza mphamvu+ kuchokera kwa Ambuye ndiponso kuchokera ku mphamvu+ zake zazikulu.