Yesaya 43:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndanena ndipo ndapulumutsa.+ Pa nthawi imene pakati panu panalibe mulungu wachilendo,+ ine ndinachititsa kuti chipulumutsocho chimveke. Choncho inuyo ndinu mboni zanga,+ ndipo ine ndine Mulungu,” akutero Yehova.+
12 “Ine ndanena ndipo ndapulumutsa.+ Pa nthawi imene pakati panu panalibe mulungu wachilendo,+ ine ndinachititsa kuti chipulumutsocho chimveke. Choncho inuyo ndinu mboni zanga,+ ndipo ine ndine Mulungu,” akutero Yehova.+