Deuteronomo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova yekha anapitiriza kumutsogolera,+Ndipo panalibe mulungu wachilendo kuwonjezera pa iye.+ Salimo 81:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakati panu sipadzakhala mulungu wosadziwika.+Ndipo simudzagwadira mulungu wachilendo.+