Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* Deuteronomo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musatsatire milungu ina, milungu iliyonse ya anthu okuzungulirani,+