Ekisodo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+ Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+ Yeremiya 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+
14 Pakuti simuyenera kugwadira mulungu wina,+ chifukwa Yehova, amene dzina lake ndi Nsanje, alidi Mulungu wansanje.*+
19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+
6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+