Yoswa 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+ Salimo 68:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+
11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+
27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+