1 Mafumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtumiki wanune ndili pakati pa anthu anu amene mwawasankha,+ anthu ochuluka zedi amene sangatheke kuwerengeka chifukwa chochuluka.+ 1 Mbiri 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+ Salimo 115:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzakuchulukitsani,+Inu ndi ana anu.+
8 Mtumiki wanune ndili pakati pa anthu anu amene mwawasankha,+ anthu ochuluka zedi amene sangatheke kuwerengeka chifukwa chochuluka.+
23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+