Genesis 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa padziko lapansi, kotero kuti ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbewu yako idzatha kuwerengedwa.+ Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+
16 Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa padziko lapansi, kotero kuti ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbewu yako idzatha kuwerengedwa.+
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+