Deuteronomo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Nkhani ya munthu wopha mnzake amene angathawire kumeneko kuti akhale ndi moyo, izikhala yotere: Akapha munthu mosadziwa ndipo sanali kudana naye,+
4 “Nkhani ya munthu wopha mnzake amene angathawire kumeneko kuti akhale ndi moyo, izikhala yotere: Akapha munthu mosadziwa ndipo sanali kudana naye,+