Ekisodo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu.+ Musagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo wokhala mumzinda wanu.+ Ekisodo 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzigwira ntchito masiku 6.+ Koma tsiku la 7 usamagwire ntchito, kuti ng’ombe yako ndi bulu wako zizipuma, ndipo mwana wa kapolo wako wamkazi ndi mlendo azipumula.+ Levitiko 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+
10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu.+ Musagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo wokhala mumzinda wanu.+
12 “Uzigwira ntchito masiku 6.+ Koma tsiku la 7 usamagwire ntchito, kuti ng’ombe yako ndi bulu wako zizipuma, ndipo mwana wa kapolo wako wamkazi ndi mlendo azipumula.+
22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+