Deuteronomo 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu.
33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu.